LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 9
  • Yehova ni “Tate wa Ana Amasiye”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova ni “Tate wa Ana Amasiye”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2025-2026 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • “Sankhani . . . Amene Mukufuna Kum’tumikila”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 9
M’bale wacicepele amene ali m’nkhani yakuti “Mungatumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo Anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino,” akuceza na m’bale wokhwima mwauzimu pamene akulalikila pamodzi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Yehova ni “Tate wa Ana Amasiye”

Caka ciliconse, acicepele ambili amasankha kukhala mabwenzi a Yehova. (Sal. 110:3) Yehova amasamala kwambili za aliyense wa inu acicepele. Amamvetsa mavuto amene mukukumana nawo, ndipo walonjeza kuti adzakuthandizani kumutumikila. Ngati muli m’banja la kholo limodzi, kumbukilani kuti Yehova ni “Tate wa ana amasiye.” (Sal. 68:5) Yehova adzakuphunzitsani, moti mudzakwanitsa kumutumikila mosasamala kanthu mmene zinthu zilili pa nyumba panu.—1 Pet. 5:10.

Cithunzi cocokela m’vidiyo yakuti “Omenya Nkhondo Yacikhulupililo Mwacipambano—Amene Akuleledwa na Kholo Limodzi.” Tammy Ludlow.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI OMENYA NKHONDO YACIKHULUPILILO MWACIPAMBANO—AMENE AKULELEDWA NA KHOLO LIMODZI, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi tiphunzilapo ciyani pa zitsanzo za Tammy, Charles, na Jimmy?

  • Kodi pa Salimo 27:10 pali mfundo yotani yolimbikitsa kwa ana amene akuleledwa na kholo limodzi?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani