LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 January tsa. 10
  • February 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 January tsa. 10

FEBRUARY 5-11

MASALIMO 1-4

Nyimbo 150 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Khalani ku Mbali ya Ufumu wa Mulungu

(Mph. 10)

[Tambitsani VIDIYO yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Masalimo.]

Maboma a anthu adzipanga okha kukhala adani a Ufumu wa Mulungu (Sal. 2:2; w21.09 15 ¶8)

Yehova akupatsa anthu onse mpata wakuti asankhe kukhala ku mbali ya Ufumu wake (Sal. 2:​10-12)

Zithunzi: 1. Gulu la anthu okwiya atanyamula zikwangwani ndipo akucita cionetselo. 2. Munthu akukuwa mokondwa ndipo wanyamula mbendela pa nthawi ya maseŵela. 3. Mwana wa sukulu akuimba nyimbo ya fuko. 4. Msilikali wanyamula mfuti. 5. Atsogoleli aŵili andale akucita kampeni. 6. Mzimayi akuponya voti m’bokosi lovotela.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndine wotsimikiza kusakhalila mbali pa ndale za dziko, ngakhale kuti zimenezi zinganibweletsele mavuto?’—w16.04 29 ¶11.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 1:4—Kodi anthu oipa ali ngati “mankhusu amene amauluzika ndi mphepo” m’lingalilo lotani? (it-1 425)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 3:1–4:8 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kukamba Mwacibadwa—Mmene Filipo anacitila zimenezi

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO yakuti kenako kambilanani lmd phunzilo 2 mfundo 1-2.

5. Kukamba Mwacibadwa—Tengelani Citsanzo ca Filipo

(Mph. 8) Makambilano ozikika pa lmd phunzilo 2 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 32

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu. 5 ¶9-15, bokosi pa tsa. 41

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 61 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani