LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 January masa. 8-9
  • January 29–February 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 29–February 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 January masa. 8-9

JANUARY 29–FEBRUARY 4

YOBU 40-42

Nyimbo 124 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Zimene Tiphunzilapo pa Zinacitikila Yobu

(Mph. 10)

Tizikumbukila kuti kapenyedwe kathu n’kopeleŵela polinganiza na Yehova (Yobu 42:​1-3; w10 10/15 3-4 ¶4-6)

Muzilandila uphungu wocokela kwa Yehova na gulu lake (Yobu 42:​5, 6; w17.06 25 ¶12)

Yehova amadalitsa anthu amene amakhulupilikabe pokumana na mayeso (Yobu 42:​10-12; Yak. 5:11; w22.06 25 ¶17-18)

Yobu na mkazi wake ali kumbali kwa phili ndipo akuyang’anana mwacikondi. Yobu akulata ziweto zawo komanso nyumba yawo.

Yehova anamufupa Yobu pokhala wokhulupilika

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Yobu 42:7—Pamene anzake atatu anali kumuneneza Yobu, kodi anali kuneneza ndani kwenikweni? (it-2 808)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zomwe mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Yobu 42:​1-17 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) NYUMBA NA NYUMBA. Munthuyo si wa cipembedzo cacikhristu. (lmd phunzilo 5 mfundo 3)

5. Kupanga Ophunzila

(Mph. 5) lff phunzilo 13 mfundo 6-7 komanso mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (lmd phunzilo 11 mfundo 4)

6. Nkhani

(Mph. 4) lmd zakumapeto A mfundo 2—Mutu: Dziko Lapansi Silidzawonongedwa Konse. (th phunzilo 13)

UMUYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 108

7. Thandizani Ena Kudziŵa Kuti Yehova Amaŵakonda

(Mph. 15) Kukambilana.

Cithunzi ca m’vidiyo yakuti “Tapeza Cikondi Cacikhristu m’Banja la Yehova.” Mimi na amayi ake abweletsa maluŵa na kakhadi kwa mlongo ali m’cipatala.

Timakondwela kulambila Mulungu amene ndiye cikondi. (1 Yoh. 4:​8, 16) Cikondi ca Yehova cimatipangitsa kumuyandikila na kukhalabe naye pa ubwenzi. Pokhala nkhosa zake, tonsefe timadziŵa kuti Yehova amatikonda.

Mmene timacitila zinthu na acibale athu, alambili anzathu, komanso anthu ena zimaonetsa kuti timatengela cikondi ca Yehova kapena ayi. (Yobu 6:14; 1 Yoh. 4:11) Tikamaonetsa ena cikondi, timawathandiza kumudziŵa Yehova na kumuyandikila. Koma ngati sitiwakonda, kungakhale kovuta kuti iwo akhulupililile kuti Yehova amaŵakonda.

Tambitsani VIDIYO yakuti Tapeza Cikondi Cacikhristu m’Banja la Yehova. Kenako, funsani omvela kuti:

Kodi mwaphunzila ciyani kwa Lei Lei na Mimi pa nkhani yoonetsa ena cikondi?

Kodi tingacite ciyani pothandiza alambili anzathu kumva kuti Yehova amaŵakonda?

  • Muziŵaona kuti ni nkhosa za Yehova zamtengo wapatali.—Sal. 100:3

  • Kambani nawo mowalimbikitsa.—Aef. 4:29

  • Citani nawo mwacikondi.—Mat. 7:​11, 12

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu. 5 ¶1-8, bokosi pa tsa. 39

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 126 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani