LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsa. 4
  • March 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 March tsa. 4

MARCH 11-17

SALIMO 18

Nyimbo 148 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Yehova Ndiye . . . Wopeleka Cipulumutso kwa Ine”

(Mph. 10)

Yehova ali monga thanthwe, malo a citetezo, komanso cishango (Sal. 18:1, 2; w09 5/1 14 ¶4-5)

Yehova amamva kulila kwathu kopempha thandizo (Sal. 18:6; it-2 1161 ¶7)

Yehova amacitapo kanthu kuti atithandize (Sal. 18:​16, 17; w22.04 3 ¶1)

Zithunzi: Davide akuwotha moto ndipo akusinkhasinkha mmene Yehova wakhala akumuthandizila. 1. Akumenyana na cimbalangondo. 2. Wagwada pafupi na mkango wakufa. 3. Iye wanyamula lupanga ndipo waponda pamsana pa Goliyati, yemwe wagona coyang’ana pansi.

Yehova angaticotsele mavuto amene timakumana nawo mmene nthawi zina anali kucitila kwa Davide. Koma nthawi zambili Mulungu amapeleka njila yopulumukila potipatsa mphamvu kuti tikwanitse kuwapilila mavutowo.—1 Akor. 10:13.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 18:10—N’cifukwa ciyani wamasalimo anakamba kuti Yehova wakwela pakerubi? (it-1 432 ¶2)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 18:20-39 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kukoma Mtima—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenaka kambilanani lmd phunzilo 3 mfundo 1-2.

5. Kukoma Mtima—Tengelani Citsanzo ca Yesu

(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 3 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 60

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 5)

7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya March

(Mph. 10) Tambitsani VIDIYO.

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu. 7 ¶1-8, bokosi pa tsa. 53

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 69 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani