LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsa. 5
  • March 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 March tsa. 5

MARCH 18-24

MASALIMO 19-21

Nyimbo 6 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

M’bale akuyang’ana kumwamba kodzala na nyenyezi.

1. “Zakumwamba Zikulengeza Ulemelelo wa Mulungu”

(Mph. 10)

Cilengedwe ca Yehova cimalengeza ulemelelo wake (Sal. 19:1; w04 1/1 8 ¶1-2)

Dzuŵa n’colengedwa codabwitsa (Sal. 19:4-6; w04 6/1 11 ¶8-10)

Tiyenela kuphunzila ku zinthu zimene Mulungu analenga (Mat. 6:28; g95 11/8 7 ¶3)


ZIMENE MUNGACITE PA KULAMBILA KWA PABANJA: Yang’anani zacilengedwe, kenaka kambilanani zimene mwaphunzilapo ponena za Yehova.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 19:7-9—Kodi mavesiwa aonetsa bwanji kalembedwe kaluso kandakatulo m’Ciheberi? (it-1 1073)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 19:​1-14 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAPOYELA Gaŵilani munthu kapepala komuitanila ku Cikumbutso, ndipo gwilitsani nchito jw.org kuti mupeze malo a Cikumbutso kufupi na kwawo. (lmd phunzilo 2 mfundo 3)

5. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Landilani munthu amene wabwela ku Cikumbutso cifukwa copeza kapepala ka ciitano pa khomo pake. Panganani zakuti mukayankhe mafunso amene ali nawo. (lmd phunzilo 3 mfundo 4)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila

(Mph. 5) Nkhani. ijwfq 45—Mutu: N’cifukwa Ciyani a Mboni za Yehova Mumacita Mwambo wa Mgonelo wa Ambuye Mosiyana na Zipembedzo Zina? (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 141

7. Yang’anani Cilengedwe Kuti Mulimbitse Cikhulupililo Canu

(Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:

Kodi zinthu zosiyana-siyana zacilengedwe zimalimbikitsa bwanji cikhulupililo canu mwa Mlengi?

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu. 7 ¶9-13, bokosi pa tsa. 56

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 127 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani