LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsa. 12
  • April 15-21

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 15-21
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 March tsa. 12

APRIL 15-21

MASALIMO 29-31

Nyimbo 108 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Cilango ni Njila Imene Mulungu Amationetsela Cikondi

(Mph. 10)

Yehova anabisa nkhope yake pamene Davide sanamumvele (Sal. 30:7; it-1 802 ¶3)

Davide anapempha Yehova kuti amucitile cifundo (Sal. 30:8)

Yehova anamukhululukila Davide (Sal. 30:5; w07 3/1 19 ¶1)


Salimo 30 iyenela kuti imakamba zimene zinacitika Davide ataŵelenga anthu mu Isiraeli.—2 Sam. 24:25.

Munthu wocotsedwa akupemphela mu motoka yake asanaloŵe m’Nyumba ya Ufumu.

ZOFUNIKA KUZISINKHASINKHA: Kodi munthu wocotsedwa angapindule bwanji na cilango cimeneco? Nanga angaonetse bwanji kuti analapa zenizeni?—w21.10 6 ¶18.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 31:23—Kodi munthu wodzikuza amalangidwa bwanji na Yehova mowilikiza? (w06 5/15 19 ¶12)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo ziti zothandiza zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 31:1-24 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 1) ULALIKI WAPOYELA. Mwacidule lalikilani munthu wotangwanika. (lmd phunzilo 5 mfundo 3)

5. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Onetsani mayi vidiyo ya ana, ndipo m’fotokozeleni mmene angapezele mavidiyo ena. (lmd phunzilo 3 mfundo 3)

6. Kubwelelako

(Mph. 3) ULALIKI WAPOYELA. Yambitsani phunzilo la Baibo kwa munthu amene m’mbuyomu anakana kuphunzila. (lmd phunzilo 8 mfundo 3)

7. Kupanga Ophunzila

(Mph. 4) lff phunzilo 14 mfundo 5 (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 45

8. Cifukwa Cake Timakhulupilila . . . Cikondi ca Mulungu

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:

Kodi vidiyo iyi yatiphunzitsa ciyani za cikondi ca Mulungu?

9. Ciunikilo ca 2024 ca Dipatimenti ya Mapulani na Mamangidwe

(Mph. 8) Nkhani. Tambitsani VIDIYO.

10. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 8 ¶13-21

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 99 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani