LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsa. 13
  • April 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 March tsa. 13

APRIL 22-28

MASALIMO 32-33

Nyimbo 103 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kuulula Macimo Akulu-akulu?

(Mph. 10)

Davide anapsinjika maganizo pamene anayesa kubisa macimo ake. Mwina linali chimo lokhudza Batiseba (Sal. 32:3, 4; w93 3/15 9 ¶7)

Davide anaulula chimo lake kwa Yehova ndipo anamukhululukila (Sal. 32:5; cl 262 ¶8)

Davide anakhala na mtendele wa mumtima Yehova atamukhululukila (Sal. 32:1; w01 6/1 30 ¶1)

Zithunzi: 1. M’bale wacinyamata akudziimba mlandu ndipo waika manja ake kumutu. 2. Iy akupemphela. 3. Wakumana na akulu aŵili. 4. Akumwetulila cifukwa ali na cikumbumtima coyela.

Tikacita chimo lalikulu, modzicepetsa tiyenela kuulula na kuvomeleza zolakwa zathu kwa Yehova, na kum’pempha kuti atikhululukile. Tiyenelanso kupempha thandizo kwa akulu amene angatithandize kucila mwauzimu. (Yak. 5:14-16) Tikatelo Yehova adzatitsitsimula.—Mac. 3:19.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 33:6—Kodi “mpweya wa m’kamwa” mwa Yehova n’ciyani? (w06 5/15 19 ¶13)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo ziti zothandiza zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 33:1-22 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kudzicepetsa—Mmene Paulo Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 4 mfundo 1-2.

5. Kudzicepetsa—Tengelani Citsanzo ca Paulo

(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 4 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 74

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 8 ¶22-24, bokosi pa tsa. 67

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 39 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani