LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 July tsa. 2
  • July 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 July tsa. 2

JULY 1-7

MASALIMO 57-59

Nyimbo 148 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumu Sauli waimilila pakati pa asilikali ake, ndipo akuyang’ana m’mwamba polankhula atagwila malaya ake amene adulidwa.

Mfumu Sauli na amuna amene anali naye pambuyo polephela kugwila Davide

1. Yehova Amasokoneza Olimbana na Anthu Ake

(Mph. 10)

Davide anakakamizika kuthaŵa Mfumu Sauli (1 Sam. 24:3; Sal. 57, tumawu twapamwamba)

Yehova analepheletsa ziwembu za anthu amene anali kulimbana na Davide (1 Sam. 24:​7-10, 17-22; Sal. 57:3)

Nthawi zambili ziwembu za anthu olimbana nafe sizikwanilitsa colinga cawo (Sal. 57:6; bt-CN 220-221 ¶14-15)

Kagulu ka abale na alongo amene anasamutsidwila ku Siberia.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ningaonetse bwanji kuti nimadalila Yehova pamene nikuzunzidwa?’—Sal. 57:2.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 57:7—Kodi kukhala wotsimikiza mtima kumatanthauza ciyani? (w23.07 18-19 ¶16-17)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 59:​1-17 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Khama—Mmene Paulo Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 7 mfundo 1-2.

5. Khama—Tengelani Citsanzo ca Paulo

(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 7 mfundo 3-5, komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 65

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 12 ¶1-6, bokosi pa tsa. 96

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 78 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani