LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsa. 3
  • November 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 November tsa. 3

NOVEMBER 11-17

SALIMO 106

Nyimbo 36 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Iwo Anaiwala Mulungu, Mpulumutsi Wawo”

(Mph. 10)

Aisiraeli atacita mantha, anapandukila Yehova (Eks. 14:​11, 12; Sal. 106:​7-9)

Pamene Aisiraeli anali na njala komanso ludzu, anayamba kung’ung’udzila Yehova (Eks. 15:24; 16:​3, 8; 17:​2, 3; Sal. 106:​13, 14)

Iwo atada nkhawa, anayamba kulambila mafano (Eks 32:1; Sal 106:​19-21; w18.07 20 ¶13)

Mlongo amene akufuna kupita mu ulaliki akuganizila mmene Yehova anamuthandizila kumbuyoku. Zithunzi: 1. Mlongoyu akucitidwa ubusa. 2. Iye walandila cola ca zinthu zofunikila. 3. Walandila kalata komanso cithunzi kucokela kwa mnzake.

ZOFUNIKA KUZISINKHASINKHA: Tikakumana na zovuta, kodi timapindula bwanji tikakumbukila mmene Yehova anatithandizilapo m’mbuyomu?

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 106:​36, 37—Kodi pali kugwilizana kotani pakati pa kulambila mafano na nsembe zopelekedwa ku ziŵanda? (w06-CN 7/15 13 ¶9)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 106:​21-48 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuphunzitsa M’njila Yosavuta Kumva—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 11 mfundo 1-2.

5. Kuphunzitsa M’njila Yosavuta Kumva—Tengelani Citsanzo ca Yesu

(Mph. 8) Kukambilana. Seŵenzetsani lmd phunzilo 11 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 78

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 18 ¶1-5, bokosi pa mas. 142, 144

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 77 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani