OCTOBER 27–NOVEMBER 2
MLALIKI 11-12
Nyimbo 155 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Mmene Mungakhalile Athanzi Komanso Acimwemwe
(Mph. 10)
Ngati n’zotheka, muzipeza nthawi yoothela dzuwa komanso kamphepo kayaziyazi (Mlal. 11:7, 8; g-CN 3/15 13 ¶6-7)
Muzisamalila thanzi lanu (Mlal. 11:10; w23.02 21 ¶6-7)
Koposa zonse, muzilambila Yehova ndi mtima wonse (Mlal. 12:13; w24.09 2 ¶2-3)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Mlal. 12:9, 10—Kodi lembali litiphunzitsa ciyani za anthu amene Mulungu anagwilitsa nchito kulemba Baibo? (it-E “Kuuzilidwa” ¶10)
Pa kuwelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibo
(Mph. 4) Mlal. 12:1-14 (th phunzilo 12)
4. Kubwelelako
(Mph. 3) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunzilo 8 mfundo 3)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pa makambilano apita, munthuyo anakuuzani kuti posacedwa anatayikilidwa wokondedwa wake mu imfa. (lmd phunzilo 9 mfundo 3)
6. Nkhani
(Mph. 5) lmd zakumapeto A mfundo 13—Mutu: Mulungu Amafuna Kutithandiza. (th phunzilo 20)
Nyimbo 111
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) rr mutu 5 ¶17-22 ndi bokosi 5A