DECEMBER 29, 2025–JANUARY 4, 2026
YESAYA 14-16
Nyimbo 63 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Adani a Anthu a Mulungu Adzalangidwa
(Mph. 10)
Babulo amene anali wodzikuza anali kudzawonongedwa kothelatu (Yes. 14:13-15, 22, 23; ip-1-CN 180 ¶16; 184 ¶24)
Yehova ananenelatu kuti adzaphwanya Msuri m’dziko lake (Yes. 14:24, 25; ip-1-CN 189 ¶1)
Yehova anatinso adzacititsa manyazi ulemelelo wa Mowabu (Yes. 16:13, 14; ip-1-CN 194 ¶12)
Left: C. Sappa/DeAgostini via Getty Images; right: Image © Homo Cosmicos/Shutterstock
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Yes. 14:1, 2—Lembali lati anthu a Yehova “adzagwila anthu amene anawagwila n’kupita nawo kudziko lina.” Kodi zimenezi zinacitika bwanji? (w06-CN 12/1 10 ¶11)
Pa kuwelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibo
(Mph. 4) Yes. 16:1-14 (th phunzilo 10)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunzilo 2 mfundo 5)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAPOYELA. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)
6. Nkhani
(Mph. 5) ijwbq nkhani 108—Mutu: Kodi Ulosi N’ciyani? (th phunzilo 14)
Nyimbo 2
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) rr mutu 8 ¶8-15 ndi bokosi 8A