LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w24 January tsa. 32
  • Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Tiyenela Kum’lambila Motani Mulungu Kuti Tim’kondweletse?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Tamandani Yehova Pakati pa Mpingo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kunola Luso Lathu mu Ulaliki Kuthandiza Maphunzilo Athu a Baibo Kukonzekela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Kodi Kulambila kwa Pabanja n’Ciani?
    Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
w24 January tsa. 32

MFUNDO YOTHANDIZA PA KUŴELENGA KWANU

Zimene Mungacite pa Phunzilo la Munthu Mwini Komanso pa Kulambila kwa Pabanja

Timalambila Yehova pamodzi na gulu lalikulu pa misonkhano ya mpingo, ya dela, komanso ya cigawo. Timamulambilanso monga banja komanso aliyense payekha-payekha. Pansipa pali zina mwa zinthu zimene mungacite pa phunzilo la munthu mwini komanso pa kulambila kwa pabanja:

  • Konzekelani misonkhano yampingo. Mungaphatikizepo kuimba nyimbo komanso kuthandiza aliyense m’banja kukonzekela ndemanga.

  • Ŵelengani nkhani ya m’Baibo. Kenako, onani mmene nkhaniyo yakukhudzilani kapena lembani zimene mwaphunzilapo.

  • Ŵelengani pemphelo lopezeka m’Baibo na kuona mmene lingakuthandizileni kuwongolela mapemphelo anu.

  • Onelelani vidiyo ya pa jw.org. Kenako kambilanani na ena kapena kulemba mfundo zimene mwaphunzilapo.

  • Konzekelani utumiki, mwina mungayeseze mmene muzalalikilila.

  • Onani zacilengedwe na kusinkhasinkha kapena kukambilana zimene cakuphunzitsani za Yehova.a

a Onani nkhani yakuti “Phunzilani Zambili za Yehova Poyang’ana Cilengedwe Cake” mu Nsanja ya Mlonda ya March 2023.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani