Yophunzila
MARCH 2025
NKHANI ZOPHUNZILA: MAY 5–JUNE 8, 2025
© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ndi kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa ndi zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibulo limene tagwilitsa nchito ndi Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati taonetsa losiyana. Koma pa kagwilitsidwe nchito ka zilembo izi: l, r, ŵ, w, y, komanso ma reduplications, tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.