Zamkati
November 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
DECEMBER 28, 2015–JANUARY 3, 2016
Phunzitsani Ana Anu Kutumikila Yehova
TSAMBA 3
JANUARY 4-10, 2016
Phunzitsani Ana Anu Acinyamata Kutumikila Yehova
TSAMBA 9
JANUARY 11-17, 2016
TSAMBA 16
JANUARY 18-24, 2016
Kodi ‘Mumakonda Anzanu Mmene Mumadzikondela’?
TSAMBA 21
JANUARY 25-31, 2016
Zaka 100 za Ulamulilo wa Ufumu wa Mulungu
TSAMBA 27
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Phunzitsani Ana Anu Kutumikila Yehova
▪ Phunzitsani Ana Anu Acinyamata Kutumikila Yehova
Yehova wapatsa makolo udindo wofunika kwambili. Iye amafuna kuti makolo aphunzitse ana ao kuti ayambe kum’tumikila. Nkhani ziŵilizi zifotokoza mmene makolo angatengele citsanzo ca Yesu ca mmene anali kuphunzitsila ophunzila ake. Zifotokozanso mmene angatengele citsanzo cake ca kudzicepetsa, cikondi, ndi kuzindikila.
▪ Yehova Ndi Mulungu Wacikondi
▪ Kodi ‘Mumakonda Anzanu Mmene Mumadzikondela’?
Nkhani yoyamba ionetselatu kuti Yehova ndi Mulungu wacikondi. Ifotokozanso mmene Mulungu waonetsela cikondi ku mtundu wa anthu. Nkhani yaciŵili ifotokoza mmene atumiki a Yehova amaonetsela kuti amakonda anzao.
▪ Zaka 100 za Ulamulilo wa Ufumu wa Mulungu
Nkhaniyi ionetsa zimene takhala tikugwilitsila nchito polalikila uthenga wabwino m’zaka 100 za ulamulilo wa Ufumu. Mudzasangalala kudziŵa zina mwa zida ndi njila zatsopano zimene timagwilitsila nchito polalikila. Mudzaphunzilanso za maphunzilo othandiza amene ofalitsa Ufumu akhala akulandila kwa zaka zambili.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
PACIKUTO: Woyang’anila dela ndi apainiya apadela amayenda pa bwato mu mtsinje wa Amazon. Iwo amakonda kuuza uthenga wabwino anthu a m’midzi yakutali imene ili m’mbali mwa mitsinje imene imathila madzi mu Amazon
BRAZIL
KULI ANTHU
203,067,835
OFALITSA
794,766
KULI APAINIYA
84,550
ANTHU AMENE ANAPEZEKA PA CIKUMBUTSO MU 2014