Zamkati
December 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
FEBRUARY 1-7, 2016
Yehova Mulungu Amakonda Kukamba ndi Anthu
TSAMBA 3
FEBRUARY 8-14, 2016
Baibulo Lomasulidwa Bwino Kwambili
TSAMBA 9
FEBRUARY 15-21, 2016
Gwilitsilani Nchito Bwino Lilime Lanu
TSAMBA 17
FEBRUARY 22-28, 2016
TSAMBA 23
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Yehova Mulungu Amakonda Kukamba ndi Anthu
▪ Baibulo Lomasulidwa Bwino Kwambili
Kwa zaka zambili, Yehova wakhala akukamba momasuka ndi atumiki ake m’zinenelo zosiyanasiyana. Tikambilana zimenezi m’nkhani ziŵilizi, ndipo tiphunzilanso mmene Baibulo la Dziko Latsopano lathandizila anthu kulemekeza dzina la Mulungu ndi kudziŵa cifunilo cake.
▪ Gwilitsilani Nchito Bwino Lilime Lanu
Kulankhula ndi mphatso yocokela kwa Mulungu. Nkhaniyi ifotokoza cifukwa cake tiyenela kudziŵa nthawi yabwino yokamba zinthu, zimene tiyenela kukamba, ndi mmene tiyenela kuzikambila. Itilimbikitsanso kutengela Yesu mwa kugwilitsila nchito mphatsoyi polemekeza Mulungu ndi kulimbikitsa ena.
▪ Yehova Adzakucilikizani
Tonse timadwala. Koma kodi tiyenela kuyembekezela kuti Yehova adzaticilitsa mozizwitsa monga mmene anacilitsila anthu akale? N’ciani cimene tiyenela kukumbukila munthu wina akatipatsa malangizo okhudza thanzi? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa ndi kutithandiza kupanga zosankha zabwino.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
PACIKUTO: Mpainiya wapadela akulalikila uthenga wabwino mosangalala kwa mai ndi ana ake. Mboni za Yehova zimalalikila coonadi m’Cisipanishi ndi m’Ciguarani. Izi ndi zinenelo zimene zimakambidwa ndi anthu ambili m’dzikoli
PARAGUAY
KULI ANTHU
6,800,236
OFALITSA