Zamkati
3 Kodi Mungathandize Ena Mumpingo Wanu?
MLUNGU WA MAY 2-8, 2016
6 Acinyamata—Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa?
MLUNGU WA MAY 9-15, 2016
12 Acinyamata—Kodi Mungakonzekele Bwanji Ubatizo?
Atumiki a Yehova ndife osangalala kwambili cifukwa caka ciliconse anthu oposa 250,000 amabatizidwa. Ambili amene amapanga cosankha cimeneci ndi acinyamata, ndipo ena amakhala kuti sanakwanitse zaka 13. N’ciani cinawathandiza kudziŵa kuti tsopano ndi okonzeka kubatizidwa? Kodi anakonzekela bwanji ubatizo? Nkhani ziŵilizi zidzayankha mafunso amenewa.
MLUNGU WA MAY 16-22, 2016
18 Kodi Tingalimbitse Bwanji Mgwilizano Pakati Pathu?
Yehova amatidalitsa ngati tigwilizana pocita cifunilo cake. Nkhaniyi ili ndi mfundo zimene zingatithandize kuti tizigwilizana m’banja, mumpingo, ndiponso polalikila
MLUNGU WA MAY 23-29, 2016
24 Yehova Amatsogolela Anthu Ake m’Njila ya ku Moyo
Nthawi zonse, Yehova amatsogolela anthu ake. Nkhaniyi, ifotokoza mmene Mulungu anali kupatsila anthu ake malangizo ndi malamulo atsopano nthawi zonse zinthu zikasintha. Tidzaphunzilanso zimene zingatithandize kuti tizidalila citsogozo ca Yehova.