1
Moni (1, 2)
Kuyamika Mulungu; Pemphelo la Paulo (3-11)
Uthenga wabwino unafalikila ngakhale kuti panali mabvuto (12-20)
Ndikhala ndi moyo kuti ndizitumikila Khristu, ndikamwalila ndipindula (21-26)
Makhalidwe anu azigwilizana ndi uthenga wabwino (27-30)
2
Akhristu azicita zinthu modzicepetsa (1-4)
Khristu adzicepetsa komanso akwezedwa (5-11)
Limbikilani kuti mukapulumuke (12-18)
Kutumiza Timoteyo komanso Epafurodito (19-30)
3
4
Mgwilizano, kusangalala, kuganizila zinthu zabwino (1-9)
Ayamikila mphatso zimene Afilipi anapeleka (10-20)
Moni wotsilizila (21-23)