LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g22 na. 1 tsa. 16
  • M’kope Ino ya Galamuka!

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • M’kope Ino ya Galamuka!
  • Galamuka!—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • Kodi Mungadziteteze Bwanji ku Mavuto a m’Dzikoli?
    Galamuka!—2022
  • “Mukhale Oyela”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Yehova Analenga Zamoyo pa Dziko Lapansi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Galamuka!—2022
g22 na. 1 tsa. 16

M’kope Ino ya Galamuka!

M’dziko la mavutoli, nthawi iliyonse aliyense wa ife angakumane na mavuto monga matsoka a zacilengedwe kapena mavuto ena ocititsidwa na anthu. Kodi inu na banja lanu mungadziteteze bwanji ku mavuto amenewa? Phunzilani mmene:

1 | Mungatetezele Thanzi Lanu

Zakudya zosiyanasiyana zopatsa thanzi zili pa tebulo.

2 | Mungatetezele Cuma Canu

Mmisili wa matabwa akukhoma msomali pa thabwa.

3 | Mungatetezele Ubale Wanu na Ena

Mwamuna na mkazi wake, omwe ni acikulile, akumbatilana.

4 | Mungalimbitsile Ciyembekezo Canu

Baibo yotsegula ili patebulo.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani