LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g22 na. 1 tsa. 3
  • Kodi Mungadziteteze Bwanji ku Mavuto a m’Dzikoli?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mungadziteteze Bwanji ku Mavuto a m’Dzikoli?
  • Galamuka!—2022
  • Nkhani Zofanana
  • M’kope Ino ya Galamuka!
    Galamuka!—2022
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • 2 | Tetezani Cuma Canu
    Galamuka!—2022
  • Tifunikila Dziko Labwino!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2021
Onaninso Zina
Galamuka!—2022
g22 na. 1 tsa. 3
Mzimayi amene ali na nkhawa akuyang’ana pa foni. Akuona gulu la anthu ocita cipolowe, matsoka a zacilengedwe, mayi wopanikizika na mavuto wanyamula mwana wake, kalombo ka kolonavailasi, cipinda ca odwala ku cipatala.

Mungadziteteze Bwanji ku Mavuto a m’Dzikoli?

Kodi mumaona kuti mavuto a m’dzikoli akukusoŵetsani kwambili mtendele kuposa kale lonse? Kodi zinthu zotsatilazi zimacitika kumene mukhala?

  • nkhondo

  • milili

  • matsoka a zacilengendwe

  • umphawi

  • tsankho

  • zaciwawa

Pakagwa tsoka, anthu ambili okhudzidwa amada nkhawa kwambili mpaka kutaya mtima. Ndipo ena tsoka likawagwela, amazizila m’nkhongono ndipo sakhala na mphamvu yocita ciliconse. Koma tsoka likacitika, kukhala na nkhawa kwa nthawi yaitali kapena kuzizila m’nkhongono kumangowonjezela vuto.

Mukakumana na mavuto aakulu, mumafunika kucitapo kanthu kuti muteteze okondedwa anu, thanzi lanu, cuma canu, komanso kuti mukhalebe acimwemwe.

Mungacite ciyani kuti mupilile mavuto amene mukukumana nawo?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani