LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 64
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Umoyo wa Mpainiya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Aphunzitseni Kucilimika
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 64

Nyimbo 64

Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi

(Miyambo 3:1, 2)

1. Njira yabwino ndiyo ya choonadi

Wina sangakusankhireni.

Choncho malangizo a M’lungu mverani,

Ndipo m’khulupilireni.

(KOLASI)

M’konde cho’nadi,

Chikhale chanuchanu.

Ndipo mudzakhala

Achimwemwe

Mukakonda cho’nadi.

2. Mukatumikira Mulungu mwakhama

Mudzalandira madalitso,

Komanso mudzapeza moyo wosatha,

Wamtendere ndi wabwino.

(KOLASI)

M’konde cho’nadi,

Chikhale chanuchanu.

Ndipo mudzakhala

Achimwemwe

Mukakonda cho’nadi.

3. M’maso mwa M’lungu tilitu ngati ana

Ofunika kulangizidwa.

Tiyende naye Atate wakumwamba,

Choncho tidzadalitsidwa.

(KOLASI)

M’konde cho’nadi,

Chikhale chanuchanu.

Ndipo mudzakhala

Achimwemwe

Mukakonda cho’nadi.

(Onaninso Sal. 26:3; Miy. 8:35; 15:31; Yoh. 8:31, 32.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani