LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 7 masa. 16-17
  • Kodi Yesu Anali Ndani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Yesu Anali Ndani?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 7
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kodi Yesu Khiristu N’ndani?
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Kodi Yesu Kristu Ndani?
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Kodi Yesu Kristu Ndani?
    Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 7 masa. 16-17

GAO 7

Kodi Yesu Anali Ndani?

Yehova anatumiza Yesu padziko lapansi. 1 Yohane 4:9

Yesu ali ku dzanja la manja la Mulungu kumwamba

Ngati tifuna kukondweletsa Yehova, pali wina amene tifunika kumvetsela kwa iye. Kale kwambili Yehova akalibe kulenga Adamu, analenga mngelo wamphamvu kumwamba.

Mariya ali na mimba, Yesu abadwa

M’kupita kwa nthawi, Yehova anamutumiza kuti akabadwile ku Betelehemu kwa namwali, Mariya. Mwanayo anam’patsa dzina lakuti Yesu.—Yohane 6:38.

Yesu aphunzitsa anthu za Yehova

Pamene Yesu anali munthu padziko lapansi, anaonetsa bwino-bwino makhalidwe a Mulungu. Anali wokoma mtima, wacikondi, ndi wokonda kuceza ndi anthu. Sanaope kuphunzitsa anthu coonadi ca Yehova.

Yesu anacita zabwino koma anthu anam’zonda. 1 Petulo 2:21-24

Yesu aukitsa mtsikana na kucilitsa mwamuna wodwala

Yesu anali kucilitsa odwala ndi kuukitsa anthu ena amene anafa.

Akulu-akulu acipembedzo anazonda Yesu cifukwa iye anali kuulula kuti ziphunzitso zawo ni zabodza ndi kuti makhalidwe awo ni oipa.

Yesu akwapuliwa na kuphedwa

Akulu-akulu acipembedzo anasonkhezela Aroma kuti amenye Yesu ndi kumupha.

  • N’cifukwa ciani tifunika kudziŵa za Yesu?—Yohane 17:3.

  • Kodi Yesu anali kucita ciani kumwamba akalibe kubwela padziko lapansi?—Akolose 1:15-17.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani