LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • snnw nyimbo 137 tsa. 2
  • Tilimbitseni Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tilimbitseni Mtima
  • Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Nkhani Zofanana
  • Tilimbitseni Mtima
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
    2018-2019 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • Kucotsa Mantha
    Kondani Anthu Kuti Mupange Ophunzila
  • Khalani Wolimba Mtima!
    2018-2019 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
Onaninso Zina
Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
snnw nyimbo 137 tsa. 2

Nyimbo 137

Tilimbitseni Mtima

Yopulinta

(Machitidwe. 4:29)

  1. Pamene tilalikila

    Uthenga wa Ufumu,

    Ambili amatitsutsa

    Ena amatiseka.

    Koma sitiŵayopa,

    Timvelela imwe mwekha.

    Conde tipempha mzimu wanu

    Mvelani pemphelo lathu.

    (KOLASI)

    Tithandizeni Yehova

    Mu utumiki wathu.

    Tikhale olimba mtima

    Tisayope adani.

    Pamene tiyembekeza

    Tsiku lanu Lalikulu

    Tithandizeni Yehova.

    Tipemphela.

  2. Pamene tivutitsidwa

    Ise mutithandiza.

    Ngakhale ticite mantha

    Imwe mutimvetsetsa.

    Conde tilanditseni

    Kwa adani athu onse.

    Tilankhule molimba mtima

    Pamene tilalikila.

    (KOLASI)

    Tithandizeni Yehova

    Mu utumiki wathu.

    Tikhale olimba mtima

    Tisayope adani.

    Pamene tiyembekeza

    Tsiku lanu Lalikulu

    Tithandizeni Yehova.

    Tipemphela.

(Onaninso 1 Ates. 2:2; Aheb. 10:35.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani