Kondani Yehova na Mtima Wanu Wonse
DEUTERONOMO 13:3
KUM’MAŴA
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 109 na Pemphelo
9:00 Zimene “Kukonda Mulungu Kumatanthauza”
9:15 Kukonda Yehova Kumatanthauza Kukonda M’bale Wako
9:30 “Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondela Wekha”
9:55 Nyimbo Na. 82 na Zilengezo
10:05 “Cikondi Cimakwilila Macimo Oculuka”
10:35 Kudzipatulila na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 50
KUMASANA
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 62
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Yosiilana: Tamandani Yehova Masiku Onse a Moyo Wanu
Ana
Acicepele
Acikulile
14:00 Nyimbo Na. 10 na Zilengezo
14:10 Kondani Yehova na Mtima Wanu Wonse
14:55 Nyimbo Na. 37 na Pemphelo