Kondwelani Mwa Yehova
Salimo 32:11
KUM’MAŴA
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 9 na Pemphelo
9:00 Kondwelani Mwa Yehova Ndipo Sangalalani
9:15 Khalani Acimwemwe Olo Kuti Mukumana na Mavuto
9:30 ‘Dzazidwani na Cimwemwe’ mu Ulaliki
9:55 Nyimbo Na. 76 na Zilengezo
10:05 Musalole Kuti Mitima Yanu ‘Ilemedwe’
10:35 Kudzipatulila na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 51
KUMASANA
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 111
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Yosiilana: Yehova Amatipangitsa Kukhala Acimwemwe
• Pamene Tipanga Ophunzila
• Pamene Tithandiza Akhristu Anzathu
• Pamene Tipilila Mavuto
14:00 Nyimbo Na. 2 na Zilengezo
14:10 Ikani Yehova Patsogolo Panu Nthawi Zonse
14:55 Nyimbo Na. 7 na Pemphelo