Tsiku Laciŵili
‘Menyani mwamphamvu nkhondo ya cikhulupililo’—Yuda 3
M’MAŴA
9:20 Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 57 na Pemphelo
9:40 YOSIYILANA: Kumbukilani—Anthu Opanda Cikhulupililo Angapeze Cikhulupililo!
• Anineve (Yona 3:5)
• Abale a Yesu Akuthupi (1 Akorinto 15:7)
• Anthu Ochuka (Afilipi 3:7, 8)
• Anthu Osapembedza (Aroma 10:13-15; 1 Akorinto 9:22)
10:30 Mangani Cikhulupililo mwa Kuseŵenzetsa Buku Lakuti, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (Yohane 17:3)
10:50 Nyimbo Na. 67 na Zilengezo
11:00 YOSIYILANA: Omenya Nkhondo ya Cikhulupililo Mwacipambano
• Aja Amene Mnzawo wa m’Cikwati si Mboni (Afilipi 3:17)
• Amene Akuleledwa na Kholo Limodzi (2 Timoteyo 1:5)
• Akhristu Amene Sali Pabanja (1 Akorinto 12:25)
11:45 UBATIZO: Pokhala na Cikhulupililo, Tidzapeza Moyo Wosatha! (Mateyu 17:20; Yohane 3:16; Aheberi 11:6)
12:15 Nyimbo Na. 79 na Kupumula
MASANA
13:35 Vidiyo ya Nyimbo
13:45 Nyimbo Na. 24
13:50 YOSIYILANA: Mmene Abale Athu Akuonetsela Cikhulupililo . . .
• mu Africa
• ku Asia
• ku Europe
• ku North America
• ku Oceania
• ku South America
14:15 YOSIYILANA: Loŵani Pakhomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo
• Phunzilani Cinenelo Catsopano (1 Akorinto 16:9)
• Katumikilenkoni Kumalo Osoŵa (Aheberi 11:8-10)
• Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu (1 Akorinto 4:17)
• Dzipelekeni Kukathandiza pa Nchito Zomanga za Gulu (Nehemiya 1:2, 3; 2:5)
• ‘Ikani Kenakake Pambali’ Kothandizila pa Nchito ya Yehova (1 Akorinto 16:2)
15:15 Nyimbo Na. 84 na Zilengezo
15:20 SEŴELO LA M’BAIBO: Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse— Gawo 1 (Danieli 1:1–2:49; 4:1-33)
16:20 ‘Menyani Mwamphamvu Nkhondo ya Cikhulupililo’! (Yuda 3; Miyambo 14:15; Aroma 16:17)
16:55 Nyimbo Na. 38 na Pemphelo Lothela