TSIKU LACIŴILI
“Nyadilani dzina lake loyela. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale”—Salimo 105:3
KUM’MAŴA
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 53 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu
• Kufunsa Mafunso (Yakobo 1:19)
• Lolani Mphamvu ya Mawu a Mulungu Kugwila Nchito (Aheberi 4:12)
• Kuseŵenzetsa Mafanizo Pofotokoza Mfundo Zofunika Kwambili (Mateyu 13:34, 35)
• Kukamba Mwaumoyo Pophunzitsa (Aroma 12:11)
• Kuonetsa Cifundo (1 Atesalonika 2:7, 8)
• Kuŵafika pa Mtima Anthu (Miyambo 3:1)
9:50 Nyimbo Na. 58 na Zilengezo
10:00 YOSIILANA: Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova
• Zida Zofufuzila (1 Akorinto 3:9; 2 Timoteyo 3:16, 17)
• Abale Athu (Aroma 16:3, 4; 1 Petulo 5:9)
• Pemphelo (Salimo 127:1)
10:45 UBATIZO: Mmene Ubatizo Wanu Ungakubweletseleni Cimwemwe Cacikulu (Miyambo 11:24; Chivumbulutso 4:11)
11:15 Nyimbo Na. 79 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 76
12:50 Mmene Abale Athu Akupezela Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila . . .
• mu Africa
• ku Asia
• ku Europe
• ku North America
• ku Oceania
• ku South America
13:35 YOSIILANA: Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo . . .
• Kudzidyetsa Okha Kuuzimu (Mateyu 5:3; Yohane 13:17)
• Kumapezeka pa Misonkhano (Salimo 65:4)
• Kupewa Mayanjano Oipa (Miyambo 13:20)
• Kuleka Makhalidwe Odetsa (Aefeso 4:22-24)
• Kukhala pa Ubale Wolimba na Yehova (1 Yohane 4:8, 19)
14:30 Nyimbo Na. 110 na Zilengezo
14:40 SEŴELO LA M’BAIBO: Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”—Gawo 1 (Nehemiya 1:1–6:19)
15:15 Kupanga Ophunzila Pali Pano, Kumatikonzekeletsa Kukapanga Ophunzila m’Dziko Latsopano (Yesaya 11:9; Machitidwe 24:15)
15:50 Nyimbo Na. 140 na Pemphelo Lothela