Penguins: By courtesy of John R. Peiniger
Tsiku Loyamba
“Cikondi n’coleza mtima” 1 Akorinto 13:4
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 66 na Pemphelo
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: N’cifukwa Ciyani ‘Kuleza Mtima’ N’kofunika? (Yakobo 5:7, 8; Akolose 1:9-11; 3:12)
9:10 YOSIYILANA: “Ciliconse Cili Ndi Nthawi Yake”
• Sinkhasinkhani Mmene Yehova Amaonela Nthawi (Mlaliki 3:1-8, 11)
• Kulimbitsa Ubwenzi Kumatenga Nthawi (Miyambo 17:17)
• Kukula Mwauzimu Kumatenga Nthawi (Maliko 4:26-29)
• Kukwanilitsa Colinga Kumatenga Nthawi (Mlaliki 11:4, 6)
10:05 Nyimbo Na. 143 na Zilengezo
10:15 KUŴELENGA BAIBO MONGA SEŴELO: Davide Anayembekezela pa Yehova (1 Samueli 24:2-15; 25:1-35; 26:2-12; Salimo 37:1-7)
10:45 Muziyamikila Ubwino wa Kuleza Mtima Kwakukulu kwa Yehova (Aroma 2:4, 6, 7; 2 Petulo 3:8, 9; Chivumbulutso 11:18)
11:15 Nyimbo Na. 147 na Kupumula
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 17
12:50 Tengelani Kuleza Mtima kwa Yesu (Aheberi 12:2, 3)
13:10 YOSIYILANA: Tengelani Citsanzo ca Amene Anayembekezela Malonjezo a Mulungu Moleza Mtima
• Abulahamu na Sara (Aheberi 6:12)
• Yosefe (Genesis 39:7-9)
• Yobu (Yakobo 5:11)
• Moredekai na Esitere (Esitere 4:11-16)
• Zekariya na Elizabeti (Luka 1:6, 7)
• Paulo (Machitidwe 14:21, 22)
14:10 Nyimbo Na. 11 na Zilengezo
14:20 YOSIYILANA: Zacilengedwe Zimatiphunzitsa Kuti Yehova Amasunga Nthawi
• Zomela (Mateyu 24:32, 33)
• Zolengedwa za m’Nyanja (2 Akorinto 6:2)
• Mbalame (Yeremiya 8:7)
• Tudoyo (Miyambo 6:6-8; 1 Akorinto 9:26)
• Nyama za Kumtunda (Mlaliki 4:6; Afilipi 1:9, 10)
15:20 “Simukudziŵa Tsiku Kapena Ola Lake” (Mateyu 24:36; 25:13, 46)
15:55 Nyimbo Na. 27 na Pemphelo Lothela