LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CO-pgm24 masa. 6-7
  • Tsiku Lacitatu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tsiku Lacitatu
  • Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
  • Nkhani Zofanana
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2021
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2017
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2022
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
CO-pgm24 masa. 6-7
Zithunzi: Zimene zili mu pulogilamu ya Tsiku Lothela. 1. Zekariya na Elizabeti. 2. Yosefe ali m’nyumba yocitila za ukalipentala ndipo wanyamula Yesu ali wamng’ono. 3. Yesu akuyang’ana pansi ali kumwamba.

Tsiku Lacitatu

“. . . kenako mapeto adzafika.”​—Mateyu 24:14

M’maŵa

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 84 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIYILANA: Tengelani Amene Anali na Cikhulupililo mu Uthenga Wabwino

    • • Zekariya (Aheberi 12:​5, 6)

    • • Elizabeti (1 Atesalonika 5:11)

    • • Mariya (Salimo 77:12)

    • • Yosefe (Miyambo 1:5)

    • • Simiyoni na Anna (1 Mbiri 16:34)

    • • Yesu (Yohane 8:​31, 32)

  • 10:05 Nyimbo Na. 65 na Zilengezo

  • 10:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: Cifukwa Cake Sitiopa Uthenga Woipa (Salimo 112:​1-10)

  • 10:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 11:15 Nyimbo Na. 61 na Kupumula

Masana

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 122

  • 12:50 KUŴELENGA BAIBO MONGA SEŴELO: “Nthawi Yodikila Yatha” (Chivumbulutso 10:6)

  • 13:20 Nyimbo Na. 126 na Zilengezo

  • 13:30 Kodi Mwaphunzila Ciyani?

  • 13:40 “Gwilitsitsani Uthenga Wabwino”—Cifukwa Ciyani Ndiponso Motani? (1 Akorinto 2:16; 15:​1, 2, 58; Maliko 6:​30-34)

  • 14:30 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani