Mau Oyamba
Muganiza Bwanji?
Munthu atakufunsani kuti kumwamba kuli ciani, mungayankhe bwanji?
Tingaphunzile zambili kwa Yesu cifukwa iye anati: “Ine ndine wocokela kumwamba.”—Yohane 8:23.
Magazini ino ya Nsanja ya Mlonda, ikamba zimene Yesu na Atate wake afotokoza ponena za kumwamba.