LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp17 na. 4 tsa. 16
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Baibo ingakuthandizeni kutsiliza nkhawa?
  • Kodi n’zotheka nkhawa kuthelatu?
  • Tulilani Yehova Nkhawa Zanu Zonse
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Mmene Tingathanilane Nazo Nkhawa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Nkhawa Zokhudza Ngozi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • 1 | Pemphelo—“Mutulileni Nkhawa Zanu Zonse”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
wp17 na. 4 tsa. 16
Banja lili m’Paradaiso

Mu Ufumu wa Mulungu, anthu “adzasangalala ndi mtendele woculuka.”—Salimo 37:11

Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Kodi Baibo ingakuthandizeni kutsiliza nkhawa?

Kodi mungayankhe bwanji?

  • Inde

  • Iyai

  • Kapena

Zimene Baibo imakamba

‘Tulilani [Mulungu] nkhawa zanu zonse, pakuti amakudelani nkhawa.’ (1 Petulo 5:7) Baibo imatsimikizila kuti Mulungu angakuthandizeni kutsiliza nkhawa zanu.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Pemphelo lingakuthandizeni kupeza “mtendele wa Mulungu,” umene ungacepetse nkhawa zanu.—Afilipi 4:6, 7.

  • Cina, kuŵelenga Mau a Mulungu kungakuthandizeni kulimbana ndi nkhawa. —Mateyu 11:28-30.

Kodi n’zotheka nkhawa kuthelatu?

Ena amakhulupilila kuti . . .nkhawa na kuvutika maganizo ni mbali ya umoyo wa munthu, pamene ena amakhulupilila kuti nkhawa zimakasila m’moyo wina pambuyo pa imfa. Nanga imwe muganiza bwanji?

Zimene Baibo imakamba

Mulungu adzacotsapo zinthu zonse zobweletsa nkhawa. “Imfa sidzakhalaponso. Sipadzakhalanso kulila, kapena kubuula, ngakhale kupweteka.”—Chivumbulutso 21:4.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Mu Ufumu wa Mulungu, anthu adzakhala pamtendele.—Yesaya 32:18.

  • Nkhawa zonse na kuvutika maganizo zidzaiŵalika.—Yesaya 65:17.

Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani 3 m’buku iyi, Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, yofalitsidwa na Mboni za Yehova

Buku imeneyi ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani