LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsa. 8
  • Nchito Yogaŵila Tumapepala Toitanila Anthu ku Msonkhano Wacigawo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Nchito Yogaŵila Tumapepala Toitanila Anthu ku Msonkhano Wacigawo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ZIMENE MUFUNIKA KUDZIŴA
  • KODI MUDZAKAMBA CIANI?
  • MMENE MUNGAKULITSILE CIDWI
  • Ciitano Cacindunji
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Ciitano Capadela
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Nchito Yapadela Imene Imakhala ndi Zotulukapo Zabwino
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Nchito Yoitanila Anthu ku Cikumbutso Idzayamba pa March 1
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 April tsa. 8

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

Nchito Yogaŵila Tumapepala Toitanila Anthu ku Msonkhano Wacigawo

Wa Mboni za Yehova waimilila pafupi ndi shelu ya mawilo, ndipo akulalikila mwamuna

Caka ciliconse, timayembekezela kucita phwando la kuuzimu pa misonkhano yathu yacigawo. Conco, tiyenela kuitana anthu mmene tingathele kuti adzacite nafe msonkhanowu, kuti naonso akaone kuti Yehova ndi wabwino. (Sal. 34:8) Bungwe lililonse la akulu lidzapanga makonzedwe a mmene tingagaŵile tumapepala twa ciitano tumenetu.

ZIMENE MUFUNIKA KUDZIŴA

  • Kodi msonkhano wacigawo udzacitika liti?

  • Kodi mpingo udzayamba liti kugaŵila tumapepala twa ciitano?

  • Ndi liti pamene mpingo umakumana kuti ukonzekele kupita mu ulaliki?

  • Kodi ndaika zolinga zotani ponena za kugaŵila tumapepala twa ciitano?

  • Kodi ndidzaitana ndani?

KODI MUDZAKAMBA CIANI?

Kapepala Koitanila Anthu ku Msonkhano Wacigawo wa 2016

Mukapatsana moni, mungakambe kuti:

“Tikugwila nchito yapadela imene ikucitika padziko lonse yoitanila anthu ku cocitika cofunika kwambili. Deti, nthawi, ndi malo zalembedwa pa kapepala aka ka ciitano. Tidzasangalala kuona kuti mwapezekapo.”

MMENE MUNGAKULITSILE CIDWI

Magazini a Galamukani! Na. 2 2016 | Is the Bible Just a Good Book?

Ngakhale kuti tifuna kuitanila anthu ambili ku msonkhano wacigawo, tifunika kukhala chelu kuti tithandize anthu amene aonetsa cidwi.

Kumapeto kwa mlungu, mungagaŵile magazini pamodzi ndi kapepala ka ciitano.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani