CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 26-33
Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima
Kukumbukila mmene Yehova amapulumutsila kunalimbikitsa Davide
27:1-3
Yehova anapulumutsa Davide wacicepele ku mkango
Yehova anathandiza Davide kupha cimbalangondo kuti ateteze gulu la nkhosa
Yehova anathandiza Davide kupha Goliyati
N’ciani cingatithandize kukhala wolimba mtima ngati Davide?
27:4, 7, 11
Pemphelo
Kulalikila
Kupezeka pamisonkhano
Phunzilo laumwini ndi kulambila kwa pabanja
Kulimbikitsa ena
Kukumbukila mmene Yehova anatithandizila m’nthawi yakumbuyo