LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • GALAMUKANI!
  • TUMAPEPALA TWAUTHENGA
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 1
Ofalitsa ku Malta alalikila mwamuna poseŵenzetsa kapepala kauthenga

Ofalitsa aseŵenzetsa tumapepala twauthenga mu ulaliki ku dziko la Malta

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 3 2016 | Breaking the Language Barrier

Cogaŵila: Galamukani! ino ili ndi nkhani yokondweletsa kwambili. [Patsani mwininyumba kope imodzi.]

Funso: Kodi mudziŵa kuti Mboni za Yehova zimamasulila mabuku m’zinenelo zoposa 750?

Lemba: Chiv. 14:6

GALAMUKANI!

Funso: Kodi muganiza kuti mfundo iyi ingakhale yothandiza kwa anthu a m’cikwati pamene akambilana mavuto ao?

Lemba: Yak. 1:19

Cogaŵila: [Chulani nkhani imene iyambila patsamba 10.] Nkhani ino, ifotokoza mfundo zina za m’Baibulo zogwilizana ndi nkhaniyi.

TUMAPEPALA TWAUTHENGA

Kapepala kauthenga

Funso: Onani funso ili. [Ŵelengani funso lokhala ndi mayankho ocita kusankhapo, patsamba loyamba la kapepala kauthenga.] Nanga inu muganiza bwanji?

Lemba: [Ŵelengani lemba limene lili patsamba 2 la kapepala kauthenga]

Cogaŵila: Kapepala aka kafotokoza mmene lembali lingakuthandizileni

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani