CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 38-44
Yehova Amathandiza Odwala
Atumiki okhulupilika ayenela kudalila Yehova kuti awathandize akakumana ndi mavuto
41:1-4
Davide anadwala kwambili
Davide anali kucita zinthu moganizila anthu onyozeka
Davide sanayembekezele Yehova kuti amucilitse mozizwitsa, koma kuti amulimbikitse ndi kumucilikiza
Yehova anali kuona kuti Davide ni wokhulupilika