UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khalani Okhulupilika Pamene Mukuyesedwa
Tambani vidiyo yakuti Khalani Okhulupilika Monga Yesu—Mukamayesedwa, ndiyeno yankhani mafunso aya:
Kodi Seji anakumana ndi zotani zimene zinayesa cikhulupililo cake kwa Yehova?
N’ciani cinam’thandiza Seji kukhalabe wokhulupilika?
Nanga kukhulupilika kwake kunabweletsa bwanji citamando kwa Yehova?