CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | DANIELI 7-9
Ulosi wa Danieli Unakambilatu za Kubwela kwa Mesiya
Yopulinta
9:24-27
MAWIKI 70 (ZAKA 490)
MAWIKI 7 (ZAKA 49)
455 ‘Mau . . . onena kuti Yerusalemu akonzedwenso’
406 Yerusalemu amangidwanso
MAWIKI 62 (ZAKA 434)
WIKI IMODZI (ZAKA 7)
29 Mesiya aonekela
33 Mesiya ‘aphedwa’
36 Kutha kwa mawiki 70
B.C.E./C.E.