CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 24
Khalanibe Ogalamuka m’Masiku Otsiliza Ano
Masiku ano, kufuna-funa zinthu za kuthupi kwacititsa anthu ambili kulephela kucita zinthu zauzimu. Kodi Akhristu ogalamuka mwauzimu amasiyana bwanji ndi anthu a ku dziko m’kaonedwe kawo pa nkhani ya . . .
maphunzilo apamwamba?
zosangalatsa?
nchito?
zinthu za kuthupi?