LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 6
  • Yesu Ali na Mphamvu Zokaukitsa Okondedwa Athu Amene Anamwalila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yesu Ali na Mphamvu Zokaukitsa Okondedwa Athu Amene Anamwalila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • “Mlongo Wako Adzauka”!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu Kumatanthauza Ciani kwa Ife?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • “Ine Ndili Ndi Ciyembekezo mwa Mulungu”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Akufa Adzauka Ndithu—Sitikaika Konse!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 6
Yesu aukitsa mwana wa Yairo

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 5-6

Yesu Ali na Mphamvu Zokaukitsa Okondedwa Athu Amene Anamwalila

5:38-42

  • Mayi alila pa manda a mwana wake, ndipo aganizila nthawi imene mwanayo adzaukitsidwa

    Cisoni cimene timamvela munthu amene timakonda akamwalila, sicitanthauza kuti tilibe cikhulupililo cakuti akufa adzauka (Gen. 23:2)

  • Kusinkha-sinkha nkhani za m’Baibo zokhudza ciukililo kudzalimbitsa cikhulupililo cathu cakuti m’tsogolo akufa adzauka

Kodi imwe mulaka-laka kudzalandila ndani pa nthawi ya ciukililo?

Muona kuti zinthu zidzakhala bwanji mukadzaonananso na okondedwa anu amene anamwalila?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani