LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 May tsa. 6
  • Yehova Adzakuthandiza Kukhala Wolimba Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Adzakuthandiza Kukhala Wolimba Mtima
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
    2018-2019 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • N’cifukwa Ciani Mulungu Amalola Kuti Anthufe Tizivutika?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Khalani Wolimba Mtima!
    2018-2019 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • Kucotsa Mantha
    Kondani Anthu Kuti Mupange Ophunzila
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 May tsa. 6
Kamtsikana kaciisiraeli kakukamba na mkazi wa Namani

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Yehova Adzakuthandiza Kukhala Wolimba Mtima

Ngati mumayenda ku sukulu, kodi mumayopa kulalikila na kuuza ena kuti ndimwe wa Mboni za Yehova? Ngati n’conco, mungacite ciani kuti mukhale ‘wolimba mtima’ polalikila za Yehova? (1 Ates. 2:2) Kodi imwe muli na zifukwa zanji zokhalila wolimba mtima? Pambuyo potamba vidiyo ya mutu wakuti Yehova Adzakuthandiza Kukhala Wolimba Mtima, yankhani mafunso otsatilawa:

  1. Sofiya apatsa Zoyi buku lakuti Phunzila kwa Mphunzitsi Waluso; kamnyamata ka Mboni kaŵelengela anzake a ku sukulu buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa

    Ni citsanzo citi ca m’Baibo cimene cinathandiza Sofiya kukhala wolimba mtima?

  2. Kodi Sofiya anapindula bwanji cifukwa coyesezelatu mmene angalalikilile?

  3. N’cifukwa ciani mufunika kuwalalikila anzanu a kusukulu?

  4. Ngati simuli pa sukulu, kodi vidiyo imeneyi yakuthandizani bwanji?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani