LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsa. 4
  • Phunzilamponi Kanthu pa Fanizo la Ndalama 10 za Mina

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Phunzilamponi Kanthu pa Fanizo la Ndalama 10 za Mina
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Tiphunzilapo pa Fanizo la Matalente
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Kodi Mumamvela Macenjezo?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 August tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 19-20

Phunzilamponi Kanthu pa Fanizo la Ndalama 10 za Mina

19:12-24

Mbuye, akapolo, na matumba a ndalama

Kodi mbali zosiyana-siyana za m’fanizo limeneli ziimila ciani?

  1. Mbuye akuimila Yesu

  2. Akapolo akuimila ophunzila odzozedwa a Yesu

  3. Ndalama zimene mbuye anapatsa akapolo ake, zikuimila udindo wapadela wopanga ophunzila

Fanizo limeneli lili na cenjezo la zimene zidzacitikila ophunzila odzodzedwa a Khristu, ngati ayamba kucita zinthu monga kapolo woipa. Yesu amayembekezela ophunzila ake kuseŵenzetsa mokwanila nthawi yawo, mphamvu zawo, na cuma cawo kuti apange ophunzila owonjezeleka.

Kodi tingatengele bwanji citsanzo ca Akhristu odzozedwa okhulupilika pa nchito yopanga ophunzila?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani