CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOHANE 1-2
Yesu Acita Cozizwitsa Cake Coyamba
Cozizwitsa coyamba ca Yesu citithandiza kudziŵa bwino umunthu wake. Kodi nkhani ya m’Baibo imeneyi ionetsa bwanji kuti?
Yesu sanali kukonda zosangalatsa mopambanitsa komanso anali kupatula nthawi kuti asangalale na anzake
Yesu anali woganizila ena
Yesu anali wopatsa