CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 1-2
Yehova Analenga Zamoyo pa Dziko Lapansi
1:3, 4, 6, 9, 11, 14, 20, 24, 27
Lembani zimene Yehova anacita pa tsiku lililonse la kulenga.
Tsiku Loyamba
Tsiku Laciŵili
Tsiku Lacitatu
Tsiku Lacinayi
Tsiku Lacisanu
Tsiku la 6