Mkulu wa ansembe angena m’Malo Oyela Koposa
Makambilano Acitsanzo
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu amene amamufuna-funa?
Lemba: 1 Pet. 5:6, 7
Ulalo: Kodi Mulungu amacita cidwi na aliyense wa ise kufika pati?
○● ULENDO WOBWELELAKO
Funso: Kodi Mulungu amacita cidwi na aliyense wa ise kufika pati?
Lemba: Mat. 10:29-31
Ulalo: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatimvetsetsa?