Ansembe akugwila nchito zawo pacihema
Makambilano Acitsanzo
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti malangizo otithandiza kukhala na umoyo wacimwemwe?
Lemba: Sal. 1:1, 2
Ulalo: Kodi kukonda ndalama na cuma kungasokoneze bwanji cimwemwe cathu?
○● ULENDO WOBWELELAKO
Funso: Kodi kukonda ndalama na cuma kungasokoneze bwanji cimwemwe cathu?
Lemba: 1 Tim. 6:9, 10
Ulalo: Ni mapindu ati amene timapeza tikakhala acimwemwe?