LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 2
  • Kusakhulupilika—Khalidwe Loipa Kwambili!

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kusakhulupilika—Khalidwe Loipa Kwambili!
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Anapatsa Mphamvu Samsoni
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Munthu Wamphamvu Kwambiri
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Pangani Mbili Yabwino Ndipo Isungeni
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Muzidalila Yehova Mmene Samisoni Anacitila
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 2
Samisoni wagona pa miyendo ya Delila, ndipo Delilayo akuuza munthu wina kuti abwele kudzam’gela tsitsi Samisoni.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusakhulupilika—Khalidwe Loipa Kwambili!

Delila analola kupeleka Samisoni kuti apatsidwe ndalama (Ower. 16:4, 5; w12 4/15 8 ¶4)

Delila anam’panikiza Samisoni mpaka anaulula cinsinsi cake (Ower. 16:15-18; w05 1/15 27 ¶4)

Akhristu ayenela kukhala okhulupilika m’banja komanso mumpingo (1 Ates. 2:10; w12 4/15 11-12 ¶15-16)

Yehova amadalitsa anthu amene amakhalabe okhulupilika—Sal. 18:25, 26.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani