LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 8
  • Pangani Mbili Yabwino Ndipo Isungeni

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pangani Mbili Yabwino Ndipo Isungeni
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kusakhulupilika—Khalidwe Loipa Kwambili!
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Pitilizani Kuonetsa Cikondi Cosasintha
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa “Uta”?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 8
Boazi akuyamikila Rute pamene akukunkha m’munda.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pangani Mbili Yabwino Ndipo Isungeni

Rute anacita zinthu moganizila ena (Rute 3:10; w12 10/1 22 ¶5)

Rute anali kudziŵika kuti anali “mkazi wabwino kwambili” (Rute 3:11; w12 10/1 23 ¶1)

Yehova anaona makhalidwe abwino a Rute, ndipo anam’dalitsa (Rute 4:11-13; w12 10/1 24 ¶3)

Lembani makhalidwe abwino amene mufuna kuti muzidziŵika nawo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani