LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 6
  • Muzidalila Thandizo la Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muzidalila Thandizo la Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Anacita Pangano na Davide
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova ni Mulungu Wacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzidalila Thandizo la Yehova

Yehova amamva kulila kwathu kopempha thandizo (2 Sam. 22:7)

Yehova ni wamphamvu kuposa mdani wathu aliyense (2 Sam. 22:14-18; cl 19 ¶11)

Mokhulupilika, Yehova amacitapo kanthu kuti atithandize (2 Sam. 22:26; w10 6/1 26 ¶4-6)

Zithunzi: 1. Mlongo wacitsikana wakhala pansi, ndipo wazyolika pamene amayi ake akum’kalipila kwinaku akumung’ambila mabuku. 2. Mlongo mmodzi-mmodziyo akuŵelenga Baibo . 3. Akukambilana na abale na alongo ku Nyumba ya Ufumu.

Yehova angakwanitse kuthetsa mayeso amene timakumana nawo. Komabe, nthawi zambili iye amatithandiza kupilila mayesowo poseŵenzetsa mzimu wake woyela, mawu ake, komanso abale na alongo athu acikhristu. (Sal. 55:22) Kodi tingacite ciyani kuti tilandile thandizo locokela kwa Mulungu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani