LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 7
  • Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa “Uta”?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova ni Mulungu Wacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mumapeleka Nsembe Zanu Modzimana?

Davide analangizidwa kuti akamange guwa la nsembe pa malo opunthila mbewu a Arauna (2 Sam. 24:18)

Mowoloŵa manja, Arauna anadzipeleka kupatsa Davide malo na nyama zopelekela nsembe (2 Sam. 24:21-23)

Davide sanafune kupeleka nsembe popanda kutailapo ciliconse (2 Sam. 24:24, 25; it-1 146)

Zithunzi: Njila zopelekela nsembe. 1. Abale na alongo akugwila nchito yomanga Nyumba ya Ufumu. 2. Mlongo wacikulile akuponya copeleka cake m’bokosi la zopeleka. 3. M’bale na mkazi wake akucita ulaliki wapoyela. 4. Abale na alongo akupeleka thandizo kwa okhudzidwa na tsoka linalake.

Yehova amakondwela ngati mofunitsitsa tiseŵenzetsa nthawi, mphamvu, na cuma cathu popititsa patsogolo zinthu za Ufumu. (w12 1/15 18 ¶8) Kodi mungadziikile zolinga zotani kuti muwonjezele nsembe zanu zopeleka citamando kwa Yehova?—Aheb. 13:15.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani