LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 15
  • Mpaka Pamene Akufa Adzaukitsidwa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mpaka Pamene Akufa Adzaukitsidwa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Yesu Ali na Mphamvu Zokaukitsa Okondedwa Athu Amene Anamwalila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Akufa Adzauka Ndithu—Sitikaika Konse!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 15
Mayi wakumbatila mwana wake amene waukitsidwa m’Paradaiso.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Mpaka Pamene Akufa Adzaukitsidwa

Munthu amene timam’konda akamwalila, timatonthozedwa na ciyembekezo cakuti akufa adzaukitsidwa. Ngakhale n’conco, ucimo na imfa zili ngati cophimba cimene cimatilepheletsa kupuma ife tonse. (Yes. 25:7, 8) Ici ni cimodzi mwa zinthu zimene zapangitsa kuti “cilengedwe conse cizibuula pamodzi ndi kumva zowawa.” (Aroma 8:22) N’ciyani cingatithandize kupilila imfa ya anthu amene timawakonda mpaka pamene adzaukitsidwe? M’Mawu a Mulungu muli mfundo zimene zingatithandize.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI MUNTHU AMENE TIMAM’KONDA AKAMWALILA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Ni zinthu zopweteka mtima ziti zimene Danielle komanso Masahiro na Yoshimi anakumana nazo?

  • Kodi mfundo 5 zochulidwa m’vidiyoyi zinawathandiza bwanji?

  • Kodi Gwelo lenileni la citonthozo ndani?—2 Akor. 1:3, 4

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2026)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani