LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March masa. 8-9
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2023

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2023
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • PA CITATU, MARCH 29
  • PA CINAYI, MARCH 30
  • PA CISANU, MARCH 31
  • PA CIŴELU, APRIL 1
  • PA SONDO, APRIL 2
  • PA MANDE, APRIL 3
  • PA CIŴILI, APRIL 4
  • CIKUMBUTSO (DZUŴA LIKALOŴA)
  • PA CITATU, APRIL 5
  • PA CINAYI, APRIL 6
  • PA CISANU, APRIL 7
  • Ndandanda ya 2022 ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Ndandanda ya Kuwelenga Baibulo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2025
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2025
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo Ya Cikumbutso ca 2024
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
  • Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March masa. 8-9
Yesu wanyamula mtengo wake wozunzilapo.

Ndandanda Ya Kuŵelenga Baibo Pa Nyengo Ya Cikumbutso Ca 2023

PA CITATU, MARCH 29

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 8 iyamba)

PA CINAYI, MARCH 30

Mariya akuthila mafuta onunkhila m’mutu mwa Yesu pamene iye akudya pathebulo.

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 9 iyamba)

Yesu—Ndi Njira, mutu 101

PA CISANU, MARCH 31

Yesu wakwela pabulu wamng’ono wamphongo, ndipo khamu la anthu lokondwela likuyala zovala zawo zakunja mumsewu komanso nthambi za kanjedza.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mutu 102

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 10 iyamba)

PA CIŴELU, APRIL 1

Yesu akugubuduza mathebulo a osintha ndalama mu kacisi.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mitu 103-104

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 11 iyamba)

PA SONDO, APRIL 2

Yesu na atumwi ake akuona pamene mkazi wamasiye wosauka akuponya tumakobidi tuŵili tocepa mphamvu moponya zopeleka.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mitu 105-114

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 12 iyamba)

PA MANDE, APRIL 3

Yudasi Isikariyoti na atsogoleli acipembedzo akupangila Yesu ciwembu. Kutsogolo kwawo kuli ndalama zasiliva zomwazikana.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mutu 115

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 13 iyamba)

PA CIŴILI, APRIL 4

CIKUMBUTSO (DZUŴA LIKALOŴA)

Yesu na atumwi ake okhulupilika ali pathebulo panthawi ya Mgonelo wa Ambuye.

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 14 iyamba)

Yesu—Ndi Njira, mitu 116-126

PA CITATU, APRIL 5

Yesu wapacikidwa pamtengo wozunzilapo pamodzi na munthu wina wacifwamba.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mitu 127-133

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 15 iyamba)

PA CINAYI, APRIL 6

Atsogoleli acipembedzo akupeleka pempho lawo kwa Pontiyo Pilato.

KUTULUKA KWA DZUŴA

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 16 iyamba)

PA CISANU, APRIL 7

Amayi atatu akusuzumila m’manda a Yesu.

KUTULUKA KWA DZUŴA

Yesu—Ndi Njira, mitu 134-135

KULOŴA KWA DZUŴA (Nisani 17 iyamba)

Mapu yoonetsa Yerusalemu na dela lozungulila. Malo odziŵika komanso ongoganizilidwa andandalikidwa. 1. Kacisi. 2. Munda wa Getsemane. 3. Nyumba ya Bwanamkubwa. 4. Nyumba ya Kayafa. 5. Nyumba Imene Herode Antipa Anali Kukhala. 6. Dziwe la Betesida. 7. Dziŵe la Siloamu. 8. Bwalo la Khoti Yaikulu ya Ayuda. 9. Gologota. 10. Munda wa Magazi.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani